0% found this document useful (0 votes)
37 views3 pages

Grade 4 Numeracy Test

Uploaded by

josekayivwa
Copyright
© © All Rights Reserved
We take content rights seriously. If you suspect this is your content, claim it here.
Available Formats
Download as PDF, TXT or read online on Scribd
0% found this document useful (0 votes)
37 views3 pages

Grade 4 Numeracy Test

Uploaded by

josekayivwa
Copyright
© © All Rights Reserved
We take content rights seriously. If you suspect this is your content, claim it here.
Available Formats
Download as PDF, TXT or read online on Scribd
You are on page 1/ 3

KENNETH DAVID KAUNDA PRIMARY SCHOOL

GRADE 4 NUMERACY TEST

END OF TERM 2 2024

Subtract the following

1. TH H T O 2. H T O
5 3 6 9 = + + + 4 6 9 = + +
-2 1 5 6 = + + + -1 4 5 = + +

3. 3 5 0 3 9 4. 6 6 6 7

-5 3 7 8 7 - 5 4 9

5. A company made 89,426 cars, out of which 43,219 have already been sold .How many cars remain
with the company ?

6. 2432+2338= 7. 5 6 1 0 0 + 3 6 2 1 =

8. 8 4 3 7 9. 4 7 3 9

+ 6 4 9 +2 3 6 4

10. Mrs Banda had 3385chickens and Mrs Tenga gave her 4228 extra more . How many chickens did
she have altogether?

(11) 998 (12) 11x12 = (13) 3 2 4

x 649 x1 5

(14) 54 (15 ) 36 (16) 9 (17) 37

X 23 x12 x8 x9

(18) 63 ÷ 9 = (19) 56 ÷ 8= (20) 630 ÷30= (21) 20 240

(22) 0 ÷ 220 = (23 ) Copy and complete , 6, 12, 18, , , , .

(24) Copy and complete , 8, 16, 24,32 , , , , .

(25) Copy and complete , 210, 220, 230, 240 , , , , .


KENNETH DAVID KAUNDA PRIMARY SCHOOL

GRADE 4 CINYANJA TEST

END OF TERM 2 2024

SECTION A

Masipelo

1. Za mwambo
2. Adzakuuzani
3. Kusanguluka
4. Kusokonezeka
5. Ulamuliro

SECTION B

Ikani masilabe osowa mu mizera

po ku wa pa ndi za
6. Mzinda ……………….. Lusaka ndi waukulu
7. Samalani ………………….. sankha atsogoleri
8. Kwezani anali kupita …………………………. Mtsinje
9. Nhuku ………………. aBanda zadya chimanga
10.Fotokozani zimene muli kuona …………………… cithunzithunzi

SECTION C

Ikani mau oyenera mu mizera

Nyimbo cimtali Jamula Mphamvu Udindo


11.Gule wa atsikana umacedwa ………………………………..………….
12.Magule acitika payenera kukhala ……………………………………..
13.…………………………………..….. wa ami ndi kusamalira nyumba
14.Phindu la magule ndi kubvina ndi …………………………………….
15.Anthu amakonda zinthu zo ………………………………………………
SECTION D

Lembani ziganizo moyenera ndi kuyihazopumira

16.Mkhiristu afunika kuthandizira okalamba ndi odwala


17.Mau abuku lopatulika amacepetsa ugawenga ndi umfuti
18.Akhiristu amabweretsa ciyanjano pa manja
19.Kuthandizira kumanga maukwati olimba ndi nchito ya a christu
20.Akhiristu amathandiziranso osauka ndi kuwatukula

SECTION E

Werengani nkhani ndi kuyanka mafuntso

Pofuna kuti anthu akale ndi nthanzi la mbwino pali zinthu zitali zomwe tiyenera
kucita kusamba, kucapa zobvala ndi kudya za kuda zopatsa nthanzi.

Matenda osiya-siyana amayamba cifukwa cosasamba, izi zimacitika pamene


thupi la munthu likhala litsiro.Pambuyo pake litsiro limayambitsa tizilombo
tomwe timayambitsa matenda.Zobvala zathu ziyenera kuchapidwa kawirikawiri
kuti tipewe matenda monga cifuwa ndi cimfine. Zobvala zalitsiro zingayambitse
matenda a mpere ndiponso, zingakhale ndi nsabwe. Kuti tikhale ndi umoyo
wabwino tiyenera kudya zakudya za magulu atatu.

Mafunso

1. Kodi tifunika kucita ciani kuti tikhale ndi thanzi?


2. Kuti tifunika kucita ciani tipewe matenda?
3. Kodi liu la litsiro ndi ciani?
4. Ninga matenda osiyana-siyana amayamba cifukwa ca ciani?
5. Ninga litsiro limayambitsa ciani?

You might also like

pFad - Phonifier reborn

Pfad - The Proxy pFad of © 2024 Garber Painting. All rights reserved.

Note: This service is not intended for secure transactions such as banking, social media, email, or purchasing. Use at your own risk. We assume no liability whatsoever for broken pages.


Alternative Proxies:

Alternative Proxy

pFad Proxy

pFad v3 Proxy

pFad v4 Proxy